Ekisodo 40:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mʼchihemacho udzaikemonso tebulo+ ndipo udzaikepo zinthu zake mwadongosolo. Kenako udzaikemo choikapo nyale+ nʼkuyatsa nyale zake.+
4 Mʼchihemacho udzaikemonso tebulo+ ndipo udzaikepo zinthu zake mwadongosolo. Kenako udzaikemo choikapo nyale+ nʼkuyatsa nyale zake.+