Ekisodo 40:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene Mose anali kuutsa chihema chopatulikacho, anayala pansi zitsulo zake zamphako+ ndi kukhazikapo mafelemu.+ Ndiyeno analowetsa mitengo yake yonyamulira+ ndi kuimika mizati pamalo ake.+
18 Pamene Mose anali kuutsa chihema chopatulikacho, anayala pansi zitsulo zake zamphako+ ndi kukhazikapo mafelemu.+ Ndiyeno analowetsa mitengo yake yonyamulira+ ndi kuimika mizati pamalo ake.+