Levitiko 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 kapena watola chinthu chotayika+ koma akukana kuti sanachitole, ndipo walumbira monama+ pa chilichonse chimene munthu angachite n’kuchimwa nacho,
3 kapena watola chinthu chotayika+ koma akukana kuti sanachitole, ndipo walumbira monama+ pa chilichonse chimene munthu angachite n’kuchimwa nacho,