Levitiko 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Wansembe amene waipereka monga nsembe yamachimo aziidya.+ Aziidyera kumalo oyera,+ m’bwalo+ la chihema chokumanako.
26 Wansembe amene waipereka monga nsembe yamachimo aziidya.+ Aziidyera kumalo oyera,+ m’bwalo+ la chihema chokumanako.