Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 10:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “N’chifukwa chiyani simunadye nsembe yamachimo m’malo oyera?+ Nsembe imeneyi ndi yopatulika koposa, ndipo Mulungu wakupatsani kuti munyamule zolakwa za khamu lonse, ndi kuphimba machimo a khamu lonseli pamaso pa Yehova.+

  • Numeri 18:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Gawo limenelo lizikhala lako pazopereka zopatulika koposa, ndizo nsembe zonse zotentha ndi moto. Nsembezo, zimene azibwera nazo kwa ine, ndi izi: Nsembe zawo zambewu,+ nsembe zawo zamachimo,+ nsembe zawo za kupalamula,+ ndi nsembe zawo zina zonse. Gawolo lizikhala chinthu chopatulika koposa kwa iwe ndi ana ako.

  • Ezekieli 44:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Iwowa ndi amene azidzadya nsembe yambewu, nsembe yamachimo ndi nsembe ya kupalamula.+ Chilichonse choperekedwa kwa Mulungu mu Isiraeli chidzakhala chawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena