Levitiko 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno azibweretsa kwa Yehova nsembe yake ya kupalamula+ chifukwa cha tchimo limene wachita. Azibweretsa nkhosa yaing’ono yaikazi+ kapena mbuzi yaing’ono yaikazi kuti ikhale nsembe yamachimo. Akatero wansembe aziphimba tchimo la munthuyo.+ Levitiko 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Lamulo la nsembe ya kupalamula+ lili motere: Nsembeyi ndi yopatulika koposa.+ Levitiko 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nsembe ya kupalamula ndi yofanana ndi nsembe yamachimo. Zonsezi lamulo lake ndi limodzi.+ Nyama ya nsembe yophimba machimo izikhala ya wansembe amene wapereka nsembeyo.
6 Ndiyeno azibweretsa kwa Yehova nsembe yake ya kupalamula+ chifukwa cha tchimo limene wachita. Azibweretsa nkhosa yaing’ono yaikazi+ kapena mbuzi yaing’ono yaikazi kuti ikhale nsembe yamachimo. Akatero wansembe aziphimba tchimo la munthuyo.+
7 Nsembe ya kupalamula ndi yofanana ndi nsembe yamachimo. Zonsezi lamulo lake ndi limodzi.+ Nyama ya nsembe yophimba machimo izikhala ya wansembe amene wapereka nsembeyo.