Levitiko 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Wansembe amene waipereka monga nsembe yamachimo aziidya.+ Aziidyera kumalo oyera,+ m’bwalo+ la chihema chokumanako. Levitiko 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwamuna aliyense yemwe ndi wansembe azidya nyamayo.+ Azidyera m’malo oyera. Nsembeyi ndi yopatulika koposa.+ Ezekieli 44:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iwowa ndi amene azidzadya nsembe yambewu, nsembe yamachimo ndi nsembe ya kupalamula.+ Chilichonse choperekedwa kwa Mulungu mu Isiraeli chidzakhala chawo.+
26 Wansembe amene waipereka monga nsembe yamachimo aziidya.+ Aziidyera kumalo oyera,+ m’bwalo+ la chihema chokumanako.
6 Mwamuna aliyense yemwe ndi wansembe azidya nyamayo.+ Azidyera m’malo oyera. Nsembeyi ndi yopatulika koposa.+
29 Iwowa ndi amene azidzadya nsembe yambewu, nsembe yamachimo ndi nsembe ya kupalamula.+ Chilichonse choperekedwa kwa Mulungu mu Isiraeli chidzakhala chawo.+