Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 5:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Akatero azibweretsa ufawo kwa wansembe, ndipo wansembeyo autape kudzaza dzanja limodzi kuti ukhale chikumbutso+ cha nsembeyo. Kenako autenthe paguwa lansembe pamene pali nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova.+ Imeneyi ndi nsembe yamachimo.+

  • Levitiko 6:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Wansembe amene waipereka monga nsembe yamachimo aziidya.+ Aziidyera kumalo oyera,+ m’bwalo+ la chihema chokumanako.

  • Levitiko 6:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “‘Mwamuna aliyense amene ndi wansembe azidya nyamayo.+ Ndi yopatulika koposa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena