Levitiko 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mwamuna aliyense+ mwa ana a Aroni azidya mkatewo. Limeneli ndi gawo lawo lochokera pansembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova, m’mibadwo yanu yonse mpaka kalekale.+ Chilichonse chimene chingakhudze nsembezi chidzakhala choyera.’” Numeri 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Uzilidyera m’malo oyera koposa,+ ndipo mwamuna aliyense azidyako.+ Gawo limenelo lizikhala chinthu chopatulika kwa iwe.+
18 Mwamuna aliyense+ mwa ana a Aroni azidya mkatewo. Limeneli ndi gawo lawo lochokera pansembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova, m’mibadwo yanu yonse mpaka kalekale.+ Chilichonse chimene chingakhudze nsembezi chidzakhala choyera.’”
10 Uzilidyera m’malo oyera koposa,+ ndipo mwamuna aliyense azidyako.+ Gawo limenelo lizikhala chinthu chopatulika kwa iwe.+