-
Levitiko 4:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Ndiyeno azichotsa mafuta onse a nkhosayo, monga mmene amachotsera mafuta a nkhosa yaing’ono yamphongo ya nsembe yachiyanjano. Pamenepo wansembe azitentha zinthu zimenezi paguwa lansembe pamwamba pa nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova.+ Ndipo wansembe aziphimba+ tchimo limene munthuyo wachita, ndipo azikhululukidwa.+
-