Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 29:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Utenge mafuta+ onse okuta matumbo,+ mafuta a pachiwindi,*+ impso ziwiri ndi mafuta ake, n’kuzitentha* paguwa lansembe.+

  • Levitiko 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pamenepo azipereka mbali ina ya nsembe yachiyanjanoyo monga nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova. Azipereka mafuta+ okuta matumbo, mafuta onse amene ali pamatumbo.+

  • Levitiko 6:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndipo moto wa paguwa lansembe uziyaka nthawi zonse. Usamazime. Wansembe aziponyapo nkhuni+ m’mawa uliwonse ndi kuikapo nsembe yopsereza pankhunipo. Akatero, azitentha mafuta a nsembe yachiyanjano pamotopo.+

  • Levitiko 9:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndipo mafuta,+ impso ndi mafuta a pachiwindi zimene anazitenga panyama ya nsembe yamachimo anazitentha paguwa lansembe,+ monga mmene Yehova analamulira Mose.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena