Levitiko 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamenepo wansembe azipereka mbalame imodzi monga nsembe yamachimo ndipo inayo monga nsembe yopsereza.+ Wansembe azim’phimbira machimo+ pamaso pa Yehova chifukwa cha kukha kwakeko.
30 Pamenepo wansembe azipereka mbalame imodzi monga nsembe yamachimo ndipo inayo monga nsembe yopsereza.+ Wansembe azim’phimbira machimo+ pamaso pa Yehova chifukwa cha kukha kwakeko.