Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 4:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Kenako azichotsa mafuta onse+ a mbuziyo, monga mmene amachotsera mafuta a nsembe yachiyanjano.+ Pamenepo wansembe azitentha mafutawo paguwa lansembe kuti likhale fungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.+ Ndiyeno wansembe aziphimba tchimo la munthuyo, ndipo azikhululukidwa.+

  • Levitiko 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndipo wansembeyo aziipereka kwa Yehova ndi kum’phimbira machimo, pamenepo mkaziyo azikhala woyera pa kukha magazi kwake.+ Limeneli ndi lamulo la mkazi amene wabereka mwana wamwamuna kapena wamkazi.

  • 1 Yohane 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Iye ndi nsembe+ yophimba+ machimo athu.+ Osati athu+ okha, komanso a dziko lonse lapansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena