Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “‘Koma ngati sangakwanitse kupereka nkhosa,+ azibweretsa kwa Yehova njiwa ziwiri+ kapena ana awiri a nkhunda kuti zikhale nsembe za kupalamula chifukwa cha tchimo limene wachita. Mbalame imodzi ikhale nsembe yamachimo+ ndipo inayo ikhale nsembe yopsereza.

  • Levitiko 14:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Mbalame imodzi ikhale nsembe yamachimo+ ndipo inayo ikhale nsembe yopsereza,+ azipereka imene angakwanitse pamodzi ndi nsembe yambewu. Pamenepo wansembe aziphimba machimo+ a munthu amene akudziyeretsayo pamaso pa Yehova.

  • Levitiko 15:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pamenepo wansembe azipereka nsembe mbalamezo, imodzi monga nsembe yamachimo ndipo inayo monga nsembe yopsereza.+ Wansembe azim’phimbira machimo pamaso pa Yehova chifukwa cha nthenda yake yakukhayo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena