Levitiko 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “Wansembe amene adzadzozedwa+ ndi kupatsidwa mphamvu* kuti atumikire monga wansembe,+ kulowa m’malo+ mwa bambo ake, aziphimba machimo ndipo azivala zovala za nsalu.+ Zovala zimenezo ndi zopatulika.+
32 “Wansembe amene adzadzozedwa+ ndi kupatsidwa mphamvu* kuti atumikire monga wansembe,+ kulowa m’malo+ mwa bambo ake, aziphimba machimo ndipo azivala zovala za nsalu.+ Zovala zimenezo ndi zopatulika.+