Ekisodo 28:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “Kenako uwombe mkanjo wamandalasi ndi ulusi wabwino kwambiri. Upangenso nduwira ya nsalu yabwino kwambiri,+ ndiponso uwombe lamba+ wa mkanjo. Ekisodo 39:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno anapanga nduwira+ ya nsalu yabwino kwambiri, mipango yokongola yokulunga kumutu+ ya nsalu zabwino kwambiri ndi makabudula a nsalu+ za ulusi wopota wabwino kwambiri. Levitiko 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Azivala mkanjo wopatulika wowomba,+ kabudula wansalu+ wobisa thupi lake, lamba wansalu wa pamimba,+ ndipo azikulunga kumutu kwake ndi nduwira yansalu.+ Zimenezi ndi zovala zopatulika.+ Iye azivala zimenezi atasamba thupi lonse.+
39 “Kenako uwombe mkanjo wamandalasi ndi ulusi wabwino kwambiri. Upangenso nduwira ya nsalu yabwino kwambiri,+ ndiponso uwombe lamba+ wa mkanjo.
28 Ndiyeno anapanga nduwira+ ya nsalu yabwino kwambiri, mipango yokongola yokulunga kumutu+ ya nsalu zabwino kwambiri ndi makabudula a nsalu+ za ulusi wopota wabwino kwambiri.
4 Azivala mkanjo wopatulika wowomba,+ kabudula wansalu+ wobisa thupi lake, lamba wansalu wa pamimba,+ ndipo azikulunga kumutu kwake ndi nduwira yansalu.+ Zimenezi ndi zovala zopatulika.+ Iye azivala zimenezi atasamba thupi lonse.+