Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 29:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “Zovala zopatulika+ za Aroni zidzakhala za ana ake+ obwera m’mbuyo mwake. Adzawadzoza+ ndi kuwapatsa mphamvu atavala zovala zimenezi.+

  • Levitiko 8:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Musachoke pakhomo la chihema chokumanako kwa masiku 7,+ kufikira tsiku lomaliza la kulongedwa kwanu unsembe, chifukwa kukupatsani mphamvu* kudzatenga masiku 7.+

  • Aheberi 5:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Zilinso chimodzimodzi ndi Khristu. Iye sanadzipatse yekha ulemerero+ mwa kudziika yekha kukhala mkulu wa ansembe.+ Koma amene anamupatsa+ ulemerero umenewo ndi amene analankhula zokhudza iyeyu kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala atate wako.”+

  • Aheberi 5:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 chifukwa watchulidwa mwachindunji ndi Mulungu kuti ndi mkulu wa ansembe monga mwa unsembe wa Melekizedeki.+

  • Aheberi 7:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndiyeno, ngati zikanakhala zothekadi kuti munthu akhale wangwiro+ kudzera mu unsembe wa Alevi,+ kodi pakanafunikanso kuti pakhale wansembe wina+ monga mwa unsembe wa Melekizedeki+ osati monga mwa unsembe wa Aroni? (Unsembe wa Alevi unali mbali ya Chilamulo pamene chinaperekedwa kwa anthu.)+

  • Aheberi 7:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Iyeyu wakhala wotero, osati malinga ndi zofunika za chilamulo, chimene chimadalira zinthu za padziko lapansi,+ koma malinga ndi mphamvu imene imapatsa moyo wosakhoza kuwonongeka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena