Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 3:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Chotero pamaso pake palibe munthu amene adzayesedwe wolungama+ mwa ntchito za chilamulo,+ popeza chilamulo chimachititsa kuti tidziwe uchimo molondola.+

  • Agalatiya 2:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Sindikukankhira kumbali kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu,+ chifukwa ngati munthu amakhala wolungama kudzera mwa chilamulo,+ ndiye kuti Khristu anangofa pachabe.+

  • Aheberi 7:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Pakuti Chilamulo sichinapangitse chilichonse kukhala changwiro,+ koma chiyembekezo+ chabwino kwambiri chimene anabweretsa kuwonjezera pa Chilamulocho, chinachita zimenezo. Ife tikuyandikira kwa Mulungu chifukwa cha chiyembekezo chimenecho.+

  • Aheberi 9:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Chihema chimenecho chinali chifaniziro+ cha nthawi yoikidwiratu imene tsopano yafika,+ ndipo mogwirizana ndi chifanizirocho, zonse ziwiri, mphatso ndi nsembe zimaperekedwa.+ Komabe, zimenezi sizipangitsa munthu amene akuchita utumiki wopatulikayo kukhala wangwiro+ m’chikumbumtima chake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena