Levitiko 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iye aziphimba machimo a malo opatulika+ koposa, chihema+ chokumanako ndi guwa lansembe.+ Aziphimbanso machimo a ansembe ndi a mpingo wonse wa anthu.+
33 Iye aziphimba machimo a malo opatulika+ koposa, chihema+ chokumanako ndi guwa lansembe.+ Aziphimbanso machimo a ansembe ndi a mpingo wonse wa anthu.+