Numeri 33:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Tsopano nawa malo amene ana a Isiraeli anaima pa ulendo wawo, atatuluka mu Iguputo+ m’magulu awo+ motsogoleredwa ndi Mose ndi Aroni.+
33 Tsopano nawa malo amene ana a Isiraeli anaima pa ulendo wawo, atatuluka mu Iguputo+ m’magulu awo+ motsogoleredwa ndi Mose ndi Aroni.+