Numeri 33:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Awa ndi malo amene Aisiraeli ankaima pa ulendo wawo, atatuluka mʼdziko la Iguputo+ mʼmagulu awo*+ motsogoleredwa ndi Mose komanso Aroni.+
33 Awa ndi malo amene Aisiraeli ankaima pa ulendo wawo, atatuluka mʼdziko la Iguputo+ mʼmagulu awo*+ motsogoleredwa ndi Mose komanso Aroni.+