Deuteronomo 4:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 kuti munthu wopha mnzake mwangozi,+ amene sanali kudana naye kale n’kale,+ azithawirako. Ameneyu azithawira ku umodzi mwa mizinda imeneyi ndi kukhala ndi moyo.+
42 kuti munthu wopha mnzake mwangozi,+ amene sanali kudana naye kale n’kale,+ azithawirako. Ameneyu azithawira ku umodzi mwa mizinda imeneyi ndi kukhala ndi moyo.+