Deuteronomo 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye amaperekera chiweruzo ana amasiye* ndi akazi amasiye,+ ndipo amakonda mlendo wokhala pakati panu+ moti amam’patsa mkate ndi chofunda. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:18 Yandikirani, ptsa. 113-114
18 Iye amaperekera chiweruzo ana amasiye* ndi akazi amasiye,+ ndipo amakonda mlendo wokhala pakati panu+ moti amam’patsa mkate ndi chofunda.