Deuteronomo 28:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Udzafufuzafufuza masana ngati mmene wakhungu amafufuzirafufuzira mu mdima,+ ndipo sudzapambana. Iwe wekha udzakhala wodyeredwa ndi kulandidwa zinthu nthawi zonse, popanda wokupulumutsa.+
29 Udzafufuzafufuza masana ngati mmene wakhungu amafufuzirafufuzira mu mdima,+ ndipo sudzapambana. Iwe wekha udzakhala wodyeredwa ndi kulandidwa zinthu nthawi zonse, popanda wokupulumutsa.+