Deuteronomo 28:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 “Ngati sudzatsatira mosamala mawu onse a chilamulo ichi olembedwa m’buku ili,+ kuti uziopa dzina laulemerero+ ndi lochititsa manthali,+ dzina lakuti Yehova,+ amene ndi Mulungu wako,
58 “Ngati sudzatsatira mosamala mawu onse a chilamulo ichi olembedwa m’buku ili,+ kuti uziopa dzina laulemerero+ ndi lochititsa manthali,+ dzina lakuti Yehova,+ amene ndi Mulungu wako,