2 Mafumu 15:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 M’masiku amenewo Yehova anayamba kutumiza+ Rezini+ mfumu ya Siriya, ndi Peka+ mwana wa Remaliya kuti akalimbane ndi Yuda.
37 M’masiku amenewo Yehova anayamba kutumiza+ Rezini+ mfumu ya Siriya, ndi Peka+ mwana wa Remaliya kuti akalimbane ndi Yuda.