2 Mafumu 15:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 M’chaka cha 52 cha Azariya mfumu ya Yuda, Peka+ mwana wa Remaliya+ anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya kwa zaka 20. 2 Mbiri 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero Peka+ mwana wa Remaliya+ anakapha anthu 120,000 ku Yuda tsiku limodzi. Onse amene anaphedwawo anali amuna olimba mtima. Iwo anaphedwa chifukwa chakuti anasiya Yehova+ Mulungu wa makolo awo. Yesaya 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano m’masiku a Ahazi mwana wa Yotamu mwana wa Uziya+ mfumu ya Yuda, Rezini+ mfumu ya Siriya ndi Peka+ mwana wa Remaliya mfumu ya Isiraeli, anabwera ku Yerusalemu kudzachita nkhondo koma analephera kulanda mzindawo.+
27 M’chaka cha 52 cha Azariya mfumu ya Yuda, Peka+ mwana wa Remaliya+ anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya kwa zaka 20.
6 Chotero Peka+ mwana wa Remaliya+ anakapha anthu 120,000 ku Yuda tsiku limodzi. Onse amene anaphedwawo anali amuna olimba mtima. Iwo anaphedwa chifukwa chakuti anasiya Yehova+ Mulungu wa makolo awo.
7 Tsopano m’masiku a Ahazi mwana wa Yotamu mwana wa Uziya+ mfumu ya Yuda, Rezini+ mfumu ya Siriya ndi Peka+ mwana wa Remaliya mfumu ya Isiraeli, anabwera ku Yerusalemu kudzachita nkhondo koma analephera kulanda mzindawo.+