2 Mafumu 15:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 M’masiku amenewo Yehova anayamba kutumiza+ Rezini+ mfumu ya Siriya, ndi Peka+ mwana wa Remaliya kuti akalimbane ndi Yuda. 2 Mbiri 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero Peka+ mwana wa Remaliya+ anakapha anthu 120,000 ku Yuda tsiku limodzi. Onse amene anaphedwawo anali amuna olimba mtima. Iwo anaphedwa chifukwa chakuti anasiya Yehova+ Mulungu wa makolo awo.
37 M’masiku amenewo Yehova anayamba kutumiza+ Rezini+ mfumu ya Siriya, ndi Peka+ mwana wa Remaliya kuti akalimbane ndi Yuda.
6 Chotero Peka+ mwana wa Remaliya+ anakapha anthu 120,000 ku Yuda tsiku limodzi. Onse amene anaphedwawo anali amuna olimba mtima. Iwo anaphedwa chifukwa chakuti anasiya Yehova+ Mulungu wa makolo awo.