2 Mafumu 15:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 M’masiku amenewo Yehova anayamba kutumiza+ Rezini+ mfumu ya Siriya, ndi Peka+ mwana wa Remaliya kuti akalimbane ndi Yuda. Yesaya 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano m’masiku a Ahazi mwana wa Yotamu mwana wa Uziya+ mfumu ya Yuda, Rezini+ mfumu ya Siriya ndi Peka+ mwana wa Remaliya mfumu ya Isiraeli, anabwera ku Yerusalemu kudzachita nkhondo koma analephera kulanda mzindawo.+
37 M’masiku amenewo Yehova anayamba kutumiza+ Rezini+ mfumu ya Siriya, ndi Peka+ mwana wa Remaliya kuti akalimbane ndi Yuda.
7 Tsopano m’masiku a Ahazi mwana wa Yotamu mwana wa Uziya+ mfumu ya Yuda, Rezini+ mfumu ya Siriya ndi Peka+ mwana wa Remaliya mfumu ya Isiraeli, anabwera ku Yerusalemu kudzachita nkhondo koma analephera kulanda mzindawo.+