2 Mafumu 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 M’chaka cha 17 cha Peka mwana wa Remaliya, Ahazi+ mwana wa Yotamu mfumu ya Yuda anakhala mfumu. 2 Mbiri 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ahazi+ anali ndi zaka 20 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 16.+ Iye sanachite zoyenera pamaso pa Yehova monga anachitira Davide kholo lake.+
28 Ahazi+ anali ndi zaka 20 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 16.+ Iye sanachite zoyenera pamaso pa Yehova monga anachitira Davide kholo lake.+