1 Mbiri 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano nawa anthu amene anapita kwa Davide ku Zikilaga,+ pa nthawi imene iye sanali kuyenda momasuka chifukwa choopa Sauli+ mwana wa Kisi. Iwowa anali ena mwa amuna amphamvu+ amene anamuthandiza pankhondo.
12 Tsopano nawa anthu amene anapita kwa Davide ku Zikilaga,+ pa nthawi imene iye sanali kuyenda momasuka chifukwa choopa Sauli+ mwana wa Kisi. Iwowa anali ena mwa amuna amphamvu+ amene anamuthandiza pankhondo.