1 Mbiri 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Amenewa anali a fuko la Gadi,+ atsogoleri a asilikali. Wamng’ono wa iwo akanatha kulimbana ndi asilikali 100, ndipo wamkulu wa iwo akanatha kulimbana ndi asilikali 1,000.+
14 Amenewa anali a fuko la Gadi,+ atsogoleri a asilikali. Wamng’ono wa iwo akanatha kulimbana ndi asilikali 100, ndipo wamkulu wa iwo akanatha kulimbana ndi asilikali 1,000.+