1 Mbiri 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho Davide anapita ku Baala-perazimu,+ ndipo anapha Afilisiti kumeneko. Atatero, Davide anati: “Mulungu woona wawononga adani anga ngati madzi achigumula pogwiritsa ntchito dzanja langa.” N’chifukwa chake malowo+ anawatcha Baala-perazimu. 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:11 Nsanja ya Olonda,6/1/1991, ptsa. 20-21
11 Choncho Davide anapita ku Baala-perazimu,+ ndipo anapha Afilisiti kumeneko. Atatero, Davide anati: “Mulungu woona wawononga adani anga ngati madzi achigumula pogwiritsa ntchito dzanja langa.” N’chifukwa chake malowo+ anawatcha Baala-perazimu.