2 Samueli 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho Davide anapita ku Baala-perazimu,+ ndipo anapha Afilisiti kumeneko. Atatero anati: “Yehova wayenda patsogolo panga ngati madzi a chigumula ndi kuwononga adani anga.”+ N’chifukwa chake malowo anawatcha Baala-perazimu.*+
20 Choncho Davide anapita ku Baala-perazimu,+ ndipo anapha Afilisiti kumeneko. Atatero anati: “Yehova wayenda patsogolo panga ngati madzi a chigumula ndi kuwononga adani anga.”+ N’chifukwa chake malowo anawatcha Baala-perazimu.*+