1 Mbiri 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho Davide anapita ku Baala-perazimu,+ ndipo anapha Afilisiti kumeneko. Atatero, Davide anati: “Mulungu woona wawononga adani anga ngati madzi achigumula pogwiritsa ntchito dzanja langa.” N’chifukwa chake malowo+ anawatcha Baala-perazimu. Yesaya 28:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova adzaimirira monga mmene anachitira paphiri la Perazimu.+ Adzakalipa ngati mmene anachitira m’chigwa cha kufupi ndi Gibeoni+ kuti achite ntchito yake. Ntchito yakeyo ndi yodabwitsa. Adzakalipa kuti achite zochita zake. Zochita zakezo n’zachilendo.+
11 Choncho Davide anapita ku Baala-perazimu,+ ndipo anapha Afilisiti kumeneko. Atatero, Davide anati: “Mulungu woona wawononga adani anga ngati madzi achigumula pogwiritsa ntchito dzanja langa.” N’chifukwa chake malowo+ anawatcha Baala-perazimu.
21 Yehova adzaimirira monga mmene anachitira paphiri la Perazimu.+ Adzakalipa ngati mmene anachitira m’chigwa cha kufupi ndi Gibeoni+ kuti achite ntchito yake. Ntchito yakeyo ndi yodabwitsa. Adzakalipa kuti achite zochita zake. Zochita zakezo n’zachilendo.+