1 Mbiri 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Hanuni anatenga atumiki a Davide+ aja ndi kuwameta ndevu.+ Kenako anadula zovala zawo pakati moti zinalekeza m’matako,+ n’kuwauza kuti azipita.+
4 Pamenepo Hanuni anatenga atumiki a Davide+ aja ndi kuwameta ndevu.+ Kenako anadula zovala zawo pakati moti zinalekeza m’matako,+ n’kuwauza kuti azipita.+