1 Mbiri 27:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Yonatani,+ mwana wa m’bale wake wa Davide, anali phungu wanzeru+ komanso mlembi. Yehiela mwana wa Hakimoni+ ndiye anali kuyang’anira ana a mfumu.+
32 Yonatani,+ mwana wa m’bale wake wa Davide, anali phungu wanzeru+ komanso mlembi. Yehiela mwana wa Hakimoni+ ndiye anali kuyang’anira ana a mfumu.+