2 Samueli 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano Aminoni anali ndi mnzake dzina lake Yehonadabu,+ mwana wa Simeya,+ m’bale wake wa Davide. Yehonadabu anali munthu wanzeru kwambiri. 2 Samueli 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye anali kutonza+ ndi kuderera Isiraeli. Pamapeto pake Yonatani+ mwana wa Simeyi,+ m’bale wake wa Davide, anamupha.
3 Tsopano Aminoni anali ndi mnzake dzina lake Yehonadabu,+ mwana wa Simeya,+ m’bale wake wa Davide. Yehonadabu anali munthu wanzeru kwambiri.
21 Iye anali kutonza+ ndi kuderera Isiraeli. Pamapeto pake Yonatani+ mwana wa Simeyi,+ m’bale wake wa Davide, anamupha.