1 Samueli 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Jese anaitana Shama+ kuti adutse, koma Samueli anati: “Yehova sanasankhenso ameneyu.” 1 Samueli 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno ana atatu aakulu a Jese anatsatira Sauli kunkhondo.+ Mayina a ana ake atatu amene anapita kunkhondowo anali Eliyabu,+ woyamba kubadwa, Abinadabu+ mwana wake wachiwiri, ndi Shama,+ wachitatu. 1 Mbiri 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Jese anabereka mwana wake woyamba Eliyabu,+ wachiwiri Abinadabu,+ wachitatu Simeya,+
13 Ndiyeno ana atatu aakulu a Jese anatsatira Sauli kunkhondo.+ Mayina a ana ake atatu amene anapita kunkhondowo anali Eliyabu,+ woyamba kubadwa, Abinadabu+ mwana wake wachiwiri, ndi Shama,+ wachitatu.