1 Samueli 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano zimene zinachitika n’zakuti, pamene iwo anali kulowa, ndipo Samueli ataona Eliyabu,+ nthawi yomweyo anati: “Mosakayikira wodzozedwa wake waonekera pamaso pa Yehova.” 1 Samueli 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno ana atatu aakulu a Jese anatsatira Sauli kunkhondo.+ Mayina a ana ake atatu amene anapita kunkhondowo anali Eliyabu,+ woyamba kubadwa, Abinadabu+ mwana wake wachiwiri, ndi Shama,+ wachitatu. 1 Mbiri 27:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 wa Ayuda anali Elihu+ mmodzi wa abale ake a Davide,+ wa Aisakara anali Omuri mwana wa Mikayeli,
6 Tsopano zimene zinachitika n’zakuti, pamene iwo anali kulowa, ndipo Samueli ataona Eliyabu,+ nthawi yomweyo anati: “Mosakayikira wodzozedwa wake waonekera pamaso pa Yehova.”
13 Ndiyeno ana atatu aakulu a Jese anatsatira Sauli kunkhondo.+ Mayina a ana ake atatu amene anapita kunkhondowo anali Eliyabu,+ woyamba kubadwa, Abinadabu+ mwana wake wachiwiri, ndi Shama,+ wachitatu.