1 Samueli 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo, Jese anaitana Abinadabu+ kuti adutse pamaso pa Samueli, koma Samueli anati: “Yehova sanasankhenso ameneyu.” 1 Mbiri 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Jese anabereka mwana wake woyamba Eliyabu,+ wachiwiri Abinadabu,+ wachitatu Simeya,+
8 Pamenepo, Jese anaitana Abinadabu+ kuti adutse pamaso pa Samueli, koma Samueli anati: “Yehova sanasankhenso ameneyu.”