1 Samueli 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo, Jese anaitana Abinadabu+ kuti adutse pamaso pa Samueli, koma Samueli anati: “Yehova sanasankhenso ameneyu.” 1 Samueli 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno ana atatu aakulu a Jese anatsatira Sauli kunkhondo.+ Mayina a ana ake atatu amene anapita kunkhondowo anali Eliyabu,+ woyamba kubadwa, Abinadabu+ mwana wake wachiwiri, ndi Shama,+ wachitatu.
8 Pamenepo, Jese anaitana Abinadabu+ kuti adutse pamaso pa Samueli, koma Samueli anati: “Yehova sanasankhenso ameneyu.”
13 Ndiyeno ana atatu aakulu a Jese anatsatira Sauli kunkhondo.+ Mayina a ana ake atatu amene anapita kunkhondowo anali Eliyabu,+ woyamba kubadwa, Abinadabu+ mwana wake wachiwiri, ndi Shama,+ wachitatu.