1 Samueli 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Mfilisiti uja anapitiriza kunena kuti: “Ine ndikutonza+ asilikali a Isiraeli lero. Ndipatseni mwamuna woti ndimenyane naye!”+ 1 Samueli 17:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Poyankha Davide anauza Mfilisitiyo kuti: “Iwe ukubwera kwa ine ndi lupanga, mkondo ndi nthungo,+ koma ine ndikubwera kwa iwe m’dzina la Yehova wa makamu,+ Mulungu wa asilikali a Isiraeli, amene iweyo wam’tonza.+ 2 Mafumu 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+
10 Ndiyeno Mfilisiti uja anapitiriza kunena kuti: “Ine ndikutonza+ asilikali a Isiraeli lero. Ndipatseni mwamuna woti ndimenyane naye!”+
45 Poyankha Davide anauza Mfilisitiyo kuti: “Iwe ukubwera kwa ine ndi lupanga, mkondo ndi nthungo,+ koma ine ndikubwera kwa iwe m’dzina la Yehova wa makamu,+ Mulungu wa asilikali a Isiraeli, amene iweyo wam’tonza.+
22 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+