2 Mbiri 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Uziya anakwiya kwambiri+ atanyamula chiwaya chofukizira+ m’manja mwake. Atawakwiyira choncho ansembewo, khate+ linabuka+ pamphumi pake ali pamaso pa ansembewo m’nyumba ya Yehova pambali pa guwa lansembe zofukiza. 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2144
19 Koma Uziya anakwiya kwambiri+ atanyamula chiwaya chofukizira+ m’manja mwake. Atawakwiyira choncho ansembewo, khate+ linabuka+ pamphumi pake ali pamaso pa ansembewo m’nyumba ya Yehova pambali pa guwa lansembe zofukiza.