Nehemiya 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mundikumbukire,+ inu Mulungu wanga, chifukwa cha zinthu zimenezi ndipo musaiwale+ ntchito za kukoma mtima kosatha zimene ndachitira nyumba+ ya Mulungu wanga ndi onse otumikira kumeneko.
14 Mundikumbukire,+ inu Mulungu wanga, chifukwa cha zinthu zimenezi ndipo musaiwale+ ntchito za kukoma mtima kosatha zimene ndachitira nyumba+ ya Mulungu wanga ndi onse otumikira kumeneko.