Yobu 35:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yobu akatsegula pakamwa pake amalankhula zopanda pake.Amachulukitsa mawu osonyeza kuti palibe chimene akudziwa.”+
16 Yobu akatsegula pakamwa pake amalankhula zopanda pake.Amachulukitsa mawu osonyeza kuti palibe chimene akudziwa.”+