Salimo 74:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu munaphwanya mitu ya Leviyatani*+ kukhala zidutswazidutswa.Munaipereka kwa anthu monga chakudya, munaipereka kwa anthu okhala m’madera opanda madzi.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 74:14 Nsanja ya Olonda,7/15/2006, tsa. 11
14 Inu munaphwanya mitu ya Leviyatani*+ kukhala zidutswazidutswa.Munaipereka kwa anthu monga chakudya, munaipereka kwa anthu okhala m’madera opanda madzi.+