Salimo 105:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Anachita zimenezi kuti asunge malangizo ake,+Ndi kusunga malamulo ake.+Tamandani Ya, anthu inu!+