Salimo 150:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 150 Tamandani Ya, anthu inu!+Tamandani Mulungu m’malo ake oyera.+Mutamandeni m’mlengalenga mmene mumasonyeza mphamvu zake.+ Chivumbulutso 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ndinamva mawu ngati a khamu lalikulu, omveka ngati mkokomo wa madzi ambiri ndi mabingu amphamvu. Mawuwo anati: “Tamandani Ya,+ anthu inu, chifukwa Yehova* Mulungu wathu, Wamphamvuyonse,+ wayamba kulamulira monga mfumu.+
150 Tamandani Ya, anthu inu!+Tamandani Mulungu m’malo ake oyera.+Mutamandeni m’mlengalenga mmene mumasonyeza mphamvu zake.+
6 Kenako ndinamva mawu ngati a khamu lalikulu, omveka ngati mkokomo wa madzi ambiri ndi mabingu amphamvu. Mawuwo anati: “Tamandani Ya,+ anthu inu, chifukwa Yehova* Mulungu wathu, Wamphamvuyonse,+ wayamba kulamulira monga mfumu.+