Salimo 118:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ili ndi tsiku limene Yehova wapanga.+Tidzakondwera ndi kusangalala pa tsiku limeneli.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 118:24 Nsanja ya Olonda,1/1/1991, tsa. 17